Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-'Alaq — Ayah 2

96:2
خَلَقَ ٱلۡإِنسَٰنَ مِنۡ عَلَقٍ ٢
Adalenga munthu kuchokera ku magazi owundana.1
Footnotes
  • [1] Madzi ambewu ya munthu, pambuyo pokhazikika mchiberekero kwa masiku makumi anayi, amatembenuka ndikukhala magazi. Ili ndilo tanthauzo la Ayah imeneyi.