Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Bayyinah — Ayah 3

98:3
فِيهَا كُتُبٞ قَيِّمَةٞ ٣
Omwe mkati mwake muli malamulo oongoka (ofotokoza za choona).1
Footnotes
  • [1] Kapena kuti “mkati mwake muli mabuku olingana,” ndiye kuti m’Qur’an muli zophunzitsa za mabuku onse omwe Allah adavumbulutsa kwa Aneneri onse akale.