Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Bayyinah — Ayah 2

98:2
رَسُولٞ مِّنَ ٱللَّهِ يَتۡلُواْ صُحُفٗا مُّطَهَّرَةٗ ٢
(Yemwe ndi) Mtumiki wochokera kwa Allah akuwawerengera makalata oyeretsedwa (ku zonama).1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo la “Makalata oyeretsedwa kuzonama” ndi Qur’an.