Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Qasas — Ayah 4

28:4
إِنَّ فِرۡعَوۡنَ عَلَا فِي ٱلۡأَرۡضِ وَجَعَلَ أَهۡلَهَا شِيَعٗا يَسۡتَضۡعِفُ طَآئِفَةٗ مِّنۡهُمۡ يُذَبِّحُ أَبۡنَآءَهُمۡ وَيَسۡتَحۡيِۦ نِسَآءَهُمۡۚ إِنَّهُۥ كَانَ مِنَ ٱلۡمُفۡسِدِينَ ٤
Ndithu Farawo adadzikuza pa dziko, ndipo adawakhazika (anthu a m’dzikolo) m’magulumagulu; gulu lina la mwa iwo adalifooketsa (poliyesa akapolo) ndi kupha ana awo achimuna, ndi kuwasiya a moyo ana awo achikazi. Ndithu iye adali mmodzi wa oononga kwambiri.1
Footnotes
  • [1] Farawo adauzidwa ndi mlosi kuti kudzabadwa mwana mwa Aisraeli wamwamuna yemwe adzathetsa ufumu wake. Pamene adamva izi adalamula kuti makanda onse achimuna a Aisraeli aphedwe. Choncho ana amuna ongobadwa kumene amaphedwa.