Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Qasas — Ayah 5

28:5
وَنُرِيدُ أَن نَّمُنَّ عَلَى ٱلَّذِينَ ٱسۡتُضۡعِفُواْ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَنَجۡعَلَهُمۡ أَئِمَّةٗ وَنَجۡعَلَهُمُ ٱلۡوَٰرِثِينَ ٥
Ndipo tidafuna kuwachitira zabwino amene adafooketsedwa m’dziko (la Iguputo), ndi kuwachita kukhala atsogoleri ndi kuwachitanso kukhala amlowa mmalo ( a Baiti Al-Makadasi).1
Footnotes
  • [1] Chimene Allah wafuna chimachitika ngakhale anthu atayesetsa m’njira izi ndi izi kuti achizembe.