Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Fatir — Ayah 5

35:5
يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّاسُ إِنَّ وَعۡدَ ٱللَّهِ حَقّٞۖ فَلَا تَغُرَّنَّكُمُ ٱلۡحَيَوٰةُ ٱلدُّنۡيَا وَلَا يَغُرَّنَّكُم بِٱللَّهِ ٱلۡغَرُورُ ٥
E inu anthu! Ndithu lonjezo la Allah ndi loona. Choncho usakunyengeni moyo wa dziko lapansi, ngakhale mdyerekezi uja wamkulu (Iblis), asakunyengeni pa za Allah.1
Footnotes
  • [1] M’ndime iyi Allah akutichenjeza kuti tisanyengedwe ndi malangizo a Satana akuti: “Chitani mmene mungafunire, Allah Wachifundo chambiri adzakukhululukirani.”