Chewa translation

Ayah by Ayah

Tags

Download Links

Chewa translation translation for Surah Al-Balad — Ayah 5

90:5
أَيَحۡسَبُ أَن لَّن يَقۡدِرَ عَلَيۡهِ أَحَدٞ ٥
Kodi (munthu wolengedwa ndi mavutoyu) akuganiza kuti palibe amene angamuthe?1
Footnotes
  • [1] Tanthauzo lake apa nkuti munthu akuganiza kuti palibe aliyense amene angamuweruze pa zolakwa zake.