Resources
Tools
Docs
Community
FAQ
Github
Login
CMS
Resources
Tools
Docs
Credits
Community
FAQ
Github
Login
Developer Resources
Translations
Chewa translation
Chewa translation
Ayah by Ayah
Tags
Translation
Chichewa
chewa
nyanja
Download Links
Download simple.json
Download simple.sqlite
Preview
Docs
Licence
A translation of every ayah of the Quran in Chichewa, Chewa, Nyanja.
Chewa translation translation for Surah Al-Balad — Ayah 6
Jump to Ayah
[]
← Previous
Next →
90:6
يَقُولُ أَهۡلَكۡتُ مَالٗا لُّبَدًا ٦
Akunena (monyadira kuti): “Ndaononga chuma chambiri (chifukwa choletsa Chisilamu kufala).”
1
Footnotes
[1]
(Ndime 6-7) Mawu awa akunenedwa kwa okanira omwe adali kupereka chuma chawo pomenyana ndi Usilamu kapena kufuna kumupha Mneneri (s.a.w). Kenako adali kudzitama chifukwa chopereka chuma chambiri pa njirayo. Izi zikumukhudza aliyense amene akufuna kuti Chisilamu chionongeke. Ndipo iwo amaganiza kuti Allah sakudziwa za maganizo awo oipa.
Loading…
Loading…